LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 11
  • April 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • April 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 11

April 12-18

NUMERI 20-21

  • Nyimbo 114 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe Ofatsa Mukapanikizika na Mayeso”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu (Mph. 10)

    • Num. 20:23-27—Tiphunzilapo ciani tikaona mmene Aroni anacitila zinthu atapatsidwa uphungu komanso mmene Yehova anamuonela ngakhale kuti analakwa? (w14 6/15 26 ¶12)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 20:1-13 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)

  • Nkhani: (Mph. 5) g 1/15 9—Mutu: Kodi Ningalamulile Bwanji Mtima Wanga? (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 90

  • Muzikamba Mawu Olimbikitsa kwa Ena: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi kukamba mawu osalimbikitsa kapena kudandaula kumakhudza bwanji anthu ena? N’ciani cinathandiza m’bale amene taona mu vidiyo kusintha khalidwe lake?

  • Musagonje Anzanu Pokunyengelelani!: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi ya zithunzi zojambula pamanja. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi anthu ambili anzawo amawanyengelela kucita ciani? Kodi pa Ekisodo 23:2 pali malangizo otani? Ni njila zinayi ziti zimene zingatithandize ngati anzathu amatinyengelela kucita zoipa?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 31

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 10 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani