LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 3
  • May 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 3

May 10-16

NUMERI 30–31

  • Nyimbo 51 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muzikwanilitsa Malumbilo Anu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 30:10-12—Tidziŵa bwanji kuti Elikana anavomeleza lumbilo la Hana lakuti adzapeleka Samueli kwa Yehova kuti azikam’tumikila? (it-2 28 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 30:1-16 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Colinga ca Mulungu—Yes. 55:11. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa cophunzitsila Baibo na kuyambitsa phunzilo. (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 5

  • Zolengedwa Zimatiphunzitsa Kupilila: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani mafunso otsatilawa pa comela, nyama, na couluka ciliconse cimene cili mu vidiyoyi: Kodi colengedwa cimeneci citiphunzitsa ciani pa nkhani ya kupilila? Tingaonetse bwanji kupilila kotelo mu umoyo wathu monga Akhristu?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 36

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 50 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani