LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 4
  • May 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 4

May 17-23

NUMERI 32–33

  • Nyimbo 142 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mukapitikitse Anthu Onse a m’Dzikolo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 33:54—Kodi malo anali kugaŵidwa bwanji ku mafuko a Isiraeli? (it-1 359 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 32:28-42 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Seŵenzetsani Mafanizo Pofotokoza Mfundo Zazikulu”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kuseŵenzetsa Mafanizo Pofotokoza Mfundo Zofunika Kwambili.

  • Nkhani: (Mph. 5) w09 10/1 30, kabokosi—Mutu: N’cifukwa Ciani Mulungu Anali Kudalitsa Nkhondo m’Nthawi ya Aisiraeli? (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 37

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 133 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani