LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 6
  • May 24-30

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 24-30
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 6

May 24-30

NUMERI 34–36

  • Nyimbo 33 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Thaŵilani kwa Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 35:31—N’cifukwa ciani Adamu na Hava sadzapindula na nsembe ya dipo la Yesu? (w91 2/15 13 ¶13)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 34:1-15 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min.) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse). (th phunzilo 9)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 2 ¶9-10 (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 88

  • Khala Bwenzi la Yehova—Cilango Ni Cikondi: (Mph. 6) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno, ngati n’kotheka, funsani mafunso ana amene munawasankhilatu. Afunseni kuti: N’cifukwa ciani nthawi zina umafunikila cilango? Kodi cilango cimakupindulitsa bwanji? N’cifukwa ciani Yehova amatipatsa cilango?

  • “Cilango Cimaonetsa Cikondi ca Yehova”: (Mph. 9) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti “Yehova Amalanga Aliyense Amene Iye Amamukonda”.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 38

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 38 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani