May 31–June 6
DEUTERONOMO 1–2
Nyimbo 125 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mulungu Ndiye Woweluza”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 1:19; 2:7—Kodi Yehova anawasamalila bwanji anthu ake pa ulendo wawo wa zaka 40 wodutsa “m’cipululu cacikulu ndi cocititsa mantha”? (w13 9/15 9 ¶9
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 1:1-18 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba makambilano acitsanzo, mwininymba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 16)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani mwininyumba kapepala koitanila anthu ku misonkhano. Ndiyeno chulani za vidiyo yakuti, N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse). (th phunzilo 11)
Nkhani: (Mph. 5) w13 8/1 14 ¶7—Mutu: Pewani Kukamba Kapena Kumvetsela Mawu Ofooketsa. (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Khalanibe Wokonzeka m’Ndime Ino Yothela ya ‘Masiku Otsiliza’”: (Mph. 15) Nkhani yokambilana yokambidwa na mkulu. Onetsani vidiyo yakuti Kodi Mwakonzekela Tsoka la Zacilengedwe?. Fotokozani zikumbutso zocokela ku ofesi ya nthambi komanso za bungwe la akulu ngati zilipo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 39
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 39 na Pemphelo