June 7-13
DEUTERONOMO 3–4
Nyimbo 98 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Malamulo a Yehova ni Anzelu Komanso Olungama”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 4:23—Kodi lamulo la palembali linali kutanthauza ciani? (w04 9/15 25 ¶3)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 3:1-13 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Kambani Mwaumoyo Pophunzitsa”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kukamba Mwaumoyo Pophunzitsa.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 5 ¶1-2 (th phunzilo 11)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 40
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 4 na Pemphelo