LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 12
  • June 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 12

June 14-20

DEUTERONOMO 5–6

  • Nyimbo 134 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Phunzitsani Ana Anu Kukonda Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 5:21—Kodi tiphunzilapo ciani pa lamulo loletsa kukhumbila mwansanje zinthu za ena? (w19.02 22 ¶11)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 5:1-21 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo. Ndiyeno, chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Sinthankoni ulaliki wanu kuti ugwilizane na zosoŵa za mwininyumba. Kenako ŵelengani lemba loyenelela. (th phunzilo 12)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 9 ¶6-7 (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 105

  • “Onetsani Cikondi m’Banja”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Onetsani Cikondi Cosatha M’banja.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 41

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 148 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani