June 21-27
DEUTERONOMO 7-8
Nyimbo 136 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Usadzacite Nawo Mgwilizano wa Ukwati”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 8:3—Kodi tiphunzilapo ciani pa cakudya ca mana cimene Yehova anapatsa Aisiraeli? (w04 2/1 13 ¶4)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 7:1-16 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Itanilani mwininyumba ku misonkhano. (th phunzilo 15)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)
Nkhani: (Mph. 5) w06 1/1 28 ¶14-15—Mutu: Musaiŵale Yehova. (th phunzilo 7)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zimene Gulu Likukwanilitsa: (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya June.
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 42
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 109 na Pemphelo