LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 May tsa. 15
  • June 28–July 4

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 28–July 4
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 May tsa. 15

June 28–July 4

DEUTERONOMO 9-10

  • Nyimbo 49 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Yehova Mulungu Wanu Akufuna Kuti Muzicita Ciani?”: (10 min.)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 9:1-3—Ngakhale kuti ana a Anaki anali “anthu amphamvu ndi aatali,” n’cifukwa ciani Aisiraeli sanafunike kuwaopa? (it-1 103)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 10:1-22 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse). (th phunzilo 9)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) fg phunzilo 12 ¶4-5 (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 135

  • Maseŵela a pa Vidiyo: Kodi Mukupambanadi?: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Kodi maseŵela a pa vidiyo angakubweletseleni mavuto otani? Ni zinthu ziti pa umoyo zimene n’zofunika kwambili kuposa maseŵela a pa vidiyo? (Aef. 5:15, 16) Kodi maseŵela a pa vidiyo amene mumasankha amaonetsa bwanji umunthu wanu wam’kati? Kodi mungacite ciani kuti mukhaledi wopambana pa umoyo?

  • “Muzipanga Zosankha Mwanzelu Pankhani ya Moŵa”: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ganizilani Zotulukapo za Kumwa Moŵa.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 43

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 44 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani