July 5-11
DEUTERONOMO 11–12
Nyimbo 40 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Yehova Amafuna Kuti Tizimulambila Motani?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 11:29—Kodi cioneka kuti vesi imeneyi inakwanilitsidwa bwanji? (it-1 925-926)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 11:1-12 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Onetsani Cifundo”: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kuonetsa Cifundo.
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak. 1: 13. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.
Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 44
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 1 na Pemphelo