LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 4
  • July 12-18

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 12-18
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 4

July 12-18

DEUTERONOMO 13–15

  • Nyimbo 38 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 14:21—Kodi tingaphunzilepo ciani pa lamulo loletsa kuŵilitsa mwana wa mbuzi mu mkaka wa make? (w06 4/1 31)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 13:1-18 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Kuvutika—1 Yoh. 5:19. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 7

  • “Musamade Nkhawa”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Cikondi Sicitha Olo Kuti . . . Ndimwe Osauka—Congo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 45

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 31 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani