LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 7
  • July 26–August 1

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 26–August 1
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 7

July 26–August 1

DEUTERONOMO 19–21

  • Nyimbo 141 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Moyo wa Munthu Ni Wamtengo Wapatali Kwa Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 21:19—N’cifukwa ciani bwalo loweluzila milandu linali kukhala pa cipata ca mzinda? (it-1 518 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 19:1-14 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso, loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) bhs 138 ¶8 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 37

  • “Yenda pa Njila Yako Popanda Cokuopseza”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Pambuyo pake, funsani mafunso awa: N’cifukwa ciani tiyenela kuyesetsa kupewa Ngozi? Ni zinthu ziti zimene tingacite kuti tipewe ngozi?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 48

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 117 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani