LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 8
  • August 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 8

August 2-8

DEUTERONOMO 22–23

  • Nyimbo 1 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Nyama”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 23:19, 20—N’cifukwa ciani Aisiraeli anali kuloledwa kulipilitsa mlendo ciwongoladzanja koma osati Mwisiraeli mnzawo? (it-1 600)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 23:1-14 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Afikeni Pamtima Anthu”: (Mph. 9) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Nolani Maluso Anu—Kuwafika Pamtima Anthu.

  • Nkhani: (Mph. 5) g 4/15 13—Mutu: Kodi Kupha Nyama N’kulakwa? (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 62

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 49

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 121 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani