August 9-15
DEUTERONOMO 24-26
Nyimbo 137 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amawadela Nkhawa Akazi”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Deut. 24:1—N’cifukwa ciani sitiyenela kuganiza kuti Cilamulo ca Mose cinapangitsa kuti cikhale cosavuta kwa mwamuna kusudzula mkazi wake? (it-1 640 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 26:4-19 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)
Ulendo Wobwelelako: (Mph.4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno, gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 2)
Nkhani: (Mph. 5) w19.06 23-24 ¶13-16—Mutu: Kodi Tingawatonthoze Bwanji na Kuwalimbikitsa Anthu Amene Anafedwa Mnzawo wa M’cikwati? (th phunzilo 20)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Akazi Acikulile Muzicita Nawo Zinthu Monga Amayi Anu, Akazi Acitsikana Monga Azilongosi Anu”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti, Onetsani Cikondi Cosatha Mumpingo—Kwa Akazi Amasiye ndi Ana Amasiye.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 50
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 150 na Pemphelo