LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 July tsa. 14
  • August 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 July tsa. 14

August 23-29

DEUTERONOMO 29-30

  • Nyimbo 3 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kutumikila Yehova Sikovuta”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut. 29:4—N’cifukwa ciani Aisiraeli ni citsanzo coticenjeza? (it-1 665 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 29:1-18 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kakhadi kongenela pa webusaiti yathu. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo, ndiyeno chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 6)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lvs 226-227 ¶3-5 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 73

  • “Kukhala Wolimba Mtima Sikovuta” (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti, Tengelani Citsanzo ca Anthu Olimba Mtima, Osati Amantha!

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 52

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 7 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2026)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani