LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 2
  • September 6-12

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 6-12
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 2

September 6-12

DEUTERONOMO 33-34

  • Nyimbo 150 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Funani Citetezo M’manja a Yehova ‘Amene Adzakhalapo Mpaka Kale-kale’”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Deut 34:6—Kodi mwina n’cifukwa ciani Yehova sanaulule kumene anaika mtembo wa Mose? (it-2 439 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Deut. 33:1-17 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—2 Tim. 3:16, 17. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo. (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 76

  • “Seŵenzetsani Buku Lakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! mu Ulaliki”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Takulandilani ku Phunzilo Lanu la Baibo. Ngati nthawi ilipo, fotokozankoni mbali zina za buku latsopano limeneli. Limbikitsani onse kuti akaŵelenge phunzilo lililonse m’buku latsopano limeneli paokha kapena pa Kulambila Kwawo kwa Pabanja.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb, phunzilo 54

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 115 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani