LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 4
  • September 13-19

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 13-19
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 4

September 13-19

YOSWA 1-2

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Mungakhalile na Moyo Wopambana”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yos. 2:4, 5—N’cifukwa ciani Rahabi anasoceletsa anthu amene mfumu inawatuma kuti akafunefune azondi? (w04 12/1 9 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 2:1-16 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Baibo—Yobu 26:7. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo. (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 56

  • “Pitilizani Kuphunzitsa Mphamvu Zanu za Kuzindikila”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti “Khalani ndi Cikumbumtima Cabwino”.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb, phunzilo 55

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 2 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani