September 20-26
YOSWA 3-5
Nyimbo 65 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yehova Amatidalitsa Ngati Ticita Zinthu Zoonetsa Cikhulupililo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Yos. 5:14, 15—Kodi timakhulupilila kuti “kalonga wa gulu lankhondo la Yehova” ndani? (w04 12/1 9 ¶2)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 3:1-13 (th phunzilo 10)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki— Seŵenzetsani Zida Zofufuzila”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova—Zida Zofufuzila.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01, ndime yoyamba na mfundo 1-2 (th phunzilo 15)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb, phunzilo 56
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 94 na Pemphelo