LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 8
  • September 27–October 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 27–October 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 8

September 27–October 3

YOSWA 6-7

  • Nyimbo 144 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pewani Zinthu Zopanda Pake”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yos. 6:20—N’ciani cionetsa kuti mzinda wa Yeriko unawonongedwa m’nthawi yocepa? (w15 11/15 15 ¶2-3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 6:1-14 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaionetse) (th phunzilo 9)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 mfundo 3 (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 121

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya September.

  • Kusamvela Mwadala Kumabweletsa Mavuto: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti ‘Palibe Ngakhale Mawu Amodzi Omwe Sanakwanilitsidwe—Kambali Kake. Ndiyeno, funsani omvetsela mafunso awa: Ni lamulo losapita m’mbali liti limene Yehova anapeleka ponena za mzinda wa Yeriko? Kodi Akani na banja lake anacita ciani? Nanga n’cifukwa ciani? Kodi tiphunzilapo ciani pa nkhaniyi? Limbikitsani onse kuti akaionelele vidiyo yonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 57

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 55 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani