LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 14
  • October 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 14

October 25-31

YOSWA 15-17

  • Nyimbo 146 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yos. 17:15, 18—Tidziŵa bwanji kuti ku Isiraeli wakale kunali nkhalango yoŵilila? (w15 7/15 32)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 15:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Itanilani munthuyo ku misonkhano. (th phunzilo 19)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 4)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 mfundo 6, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 9)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 139

  • “Lalikilani Uthenga Wabwino Wakuti Dziko Labwino Lili Pafupi!”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo ya nyimbo yopekedwa koyamba yakuti Dziko Latsopano Likubwelalo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 61

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani