LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 5
  • November 15-21

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 15-21
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 5

November 15-21

YOSWA 23-24

  • Nyimbo 50 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yos. 24:2—Kodi Tera, amene anali tate wake wa Abulahamu anali kulambila mafano? (w04 12/1 11 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yos. 24:19-33 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 2)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 20)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 01 cidule cake, mafunso obweleza, na zocita (th phunzilo 3)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 28

  • Pewani Mayanjano Oipa Kunchito: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingakulepheletseni Kukhala Okhulupilika—Mayanjano Oipa. Kenako funsani omvetsela mafunso awa: Kodi mayanjano oipa kunchito anam’khudza bwanji mlongo wa mu vidiyoyi? Ni masinthidwe otani amene anapanga? Nanga kucita zimenezo kunam’thandiza bwanji? Kodi mwaphunzilamo ciani mu vidiyo imeneyi pa nkhani ya kupewa mayanjano oipa?

  • Pezani Mabwenzi M’malo Osayembekezeleka: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Mabwenzi M’malo Osayembekezeleka. Kenako funsani omvetsela mafunso awa: Ni mavuto otani amene anapangitsa Akil kuyamba kugwilizana na anthu a makhalidwe oipa kusukulu? Kodi anapeza bwanji mabwenzi abwino mumpingo? Kodi mwaphunzila ciani mu vidiyo imeneyi pa nkhani yopeza mabwenzi abwino?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 64

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 3 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani