LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 6
  • November 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 6

November 22-28

OWERUZA 1-3

  • Nyimbo 126 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nkhani Yocititsa Cidwi Yoonetsa Kulimba Mtima”: (Mph. 10)

    Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ower. 2:10-12—N’cifukwa ciani zimenezi ni cenjezo kwa ife? (w05 1/15 24 ¶7)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ower. 3:12-31 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Landilani Thandizo la Yehova Kupitila M’pemphelo”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Pezani Cimwemwe pa Nchito Yopanga Ophunzila—Landilani Thandizo la Yehova—Pemphelo.

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 02 ndime yoyamba na mfundo 1-3 (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 53

  • Khala Bwenzi la Yehova—Uzionetsa Khalidwe Labwino mu Ulaliki: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’zotheka, pemphani ana amene munawasankhilatu kuti abwele ku pulatifomu na kuwafunsa mafunso awa: Tingakonzekele bwanji ulaliki? Kodi tingavale bwanji kuti maonekedwe athu akhale oyenela komanso osadzionetsela? Tingaonetse bwanji khalidwe labwino pamene tili mu ulaliki?

  • “Zimene Mungacite Kuti Kukumana Kotenga Malangizo a Ulaliki Kuzikhala Kopindulitsa”: (Mph. 10) Nkhani yokambilana, yokambidwa na woyang’anila utumiki. Pemphani omvetsela kuti afotokoze cifukwa cake tiyenela kufika mwamsanga pa kukumana kotenga malangizo a ulaliki.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 65

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 137 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani