LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 November tsa. 8
  • November 29–December 5, 2021

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 29–December 5, 2021
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 November tsa. 8

November 29–December 5

Oweruza 4-5

  • Nyimbo 137 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Anaseŵenzetsa Akazi Aŵili Populumutsa Anthu Ake”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ower. 5:20—Kodi nyenyezi zinamenya nkhondo motani kucokela kumwamba pothandiza Baraki? (w05 1/15 25 ¶5)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ower. 4:1-16 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani Nsanja ya Mlonda ya Na. 2 2021. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 4)

  • Nkhani: (Mph. 5) w06 3/1 28-29—Mutu: Kodi ‘akazi ayenela kukhala cete m’mipingo’ m’lingalilo lotani?—1 Akor. 14:34. (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 84

  • “Kodi Alongo Angakalamile Bwanji?”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti “Akazi Ogwila Nchito Mwakhama Potumikila Ambuye”.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 66

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 96 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani