February 21-27
1 SAMUELI 6-8
Nyimbo 9 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mfumu Yanu N’ndani?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 7:3—Kodi vesi imeneyi itiphunzitsa ciani za kutembenuka na kulapa? (w02 4/1 12 ¶13)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 7:1-14 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani magazini pofuna kuyankha funso limene mwininyumba wafunsa. (th phunzilo 12)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Itanilani mwininyumba ku misonkhano yathu. (th phunzilo 18)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 cidule cake, mafunso obweleza, na zocita (th phunzilo 20)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)
Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwezi wa March Kapena April?: (Mph. 5) Kukambilana kozikidwa mu Kabuku ka Umoyo na Utumiki ka January-February 2021, tsa. 16.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 78
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 58 na Pemphelo