LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 2
  • March 7-13

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 7-13
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 2

March 7-13

1 SAMUELI 12-13

  • Nyimbo 4 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kudzikweza Kumanyazitsa Munthu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 12:21—Kodi Aisiraeli akanatsatila bwanji “milungu yopanda pake” (kapena kuti “zinthu zacabe” BL.)? (w11 7/15 13 ¶15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 12:1-11 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Yesu—Mat. 16:16. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 1)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 04 ndime yoyamba, na mfundo 1-2 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 46

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (Mph. 5) Onetsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya March.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 80

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 69 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani