LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 March tsa. 6
  • March 28–April 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 28–April 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 March tsa. 6

March 28–April 3

1 SAMUELI 18-19

  • Nyimbo 36 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe Odzicepetsa Zinthu Zikakuyendelani Bwino”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 19:23, 24—Kodi Mfumu Sauli anacita bwanji zinthu “ngati mneneli”? (it-2 695-696)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 18:25–19:7 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • “Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Thandizani Maphunzilo a Baibo Kuleka Makhalidwe Odetsa”: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kuleka Makhalidwe Odetsa.

  • Nkhani: (Mph. 5) km 1/03 1—Mutu: Nchito Imene Imafuna Kudzicepetsa. (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 31

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 83

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 125 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani