April 25–May 1
1 SAMUELI 25–26
Nyimbo 130 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumaugwila Mtima?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu (Mph. 10)
1 Sam. 25:18, 19—N’cifukwa ciani tingakambe kuti Abigayeli sanapandukile umutu wa mwamuna wake? (ia 80 ¶16)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 25:1-13 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
“Wonjezelani Cimwemwe Canu mu Ulaliki—Thandizani Maphunzilo a Baibo Kukhala pa Ubale Wolimba na Yehova”: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Thandizani Maphunzilo Anu a Baibo Kukhala pa Ubale Wolimba na Yehova.
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 04 mfundo 4 (th phunzilo 9)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 01
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 98 na Pemphelo