LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 2
  • May 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 2

May 2-8

1 SAMUELI 27-29

  • Nyimbo 71 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mapulani a Davide a Kamenyedwe ka Nkhondo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 28:15—Kodi Sauli “anaona” ndani pa cocitikaci? (w10 1/1 20 ¶5-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 27:1-12 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Kuvutika—Yak. 1:13. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 1)

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuchulako za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 6)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 129

  • Analimbabe pa Cizunzo: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno, funsani omvetsela mafunso awa: Kodi tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca abale athu pa nthawi ya ulamulilo wa Nazi ku Germany? Tiphunzilapo ciyani pa citsanzo ca abale athu a ku Russia, komanso a m’nthawi ya ulamulilo wakale wa Soviet Union?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 02

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 94 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani