LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 3
  • May 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 3

May 9-15

1 SAMUELI 30-31

  • Nyimbo 8 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Dzilimbitseni mwa Yehova Mulungu Wanu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Sam. 30:23, 24—Kodi tiphunzilapo ciyani pa nkhaniyi? (w05 3/15 24 ¶8)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 30:1-10 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Kuvutika—1 Yoh. 5:19. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 8)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako, gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! na kuyambitsa phunzilo la Baibo m’phunzilo 01. (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 43

  • Khala Bwenzi la Yehova—Muzipemphela Nthawi Zonse: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’kotheka, funsani mafunso ana amene munawasankhilatu. Afunseni kuti: N’cifukwa ciyani muyenela kupemphela kwa Yehova? Ni nthawi iti yabwino imene mungapemphele kwa iye? Kodi mungamuuze ciyani m’pemphelo?

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 03

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 95 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani