LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 4
  • May 16-22

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 16-22
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 4

May 16-22

2 SAMUELI 1-3

  • Nyimbo 103 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Tiphunzilapo Ciyani pa Nyimbo Yochedwa ‘Uta’?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 1:26​—N’cifukwa ciyani Davide anachula Yonatani kuti “m’bale wanga”? (it-1 369 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 3:1-16 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno fotokozelani mwininyumba za pulogilamu yathu yophunzitsa Baibo kwaulele, na kum’patsa kakhadi koloŵela pa webusaiti yathu ya jw.org. (th phunzilo 20)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 04 mfundo 5, na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 107

  • “Cikondi . . . Sicikondwela ndi Zosalungama”: (Mph. 7) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili​—Sicikondwela ndi Zosalungama..

  • “Cikondi . . . Cimayembekezela Zinthu Zonse”: (Mph. 8) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili—Cimayembekezela Zinthu Zonse.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 04

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 2 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani