LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 6
  • May 23-29

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 23-29
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 6

May 23-29

2 SAMUELI 4-6

  • Nyimbo 135 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe na Mantha Oyenela Oopa Kukhumudwitsa Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 6:8, 9​—Kodi tiphunzilapo ciyani pa zimene Davide anacita ataona mkwiyo wa Yehova? (w96 4/1 29 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 4:1-12 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako chulani za vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

  • Nkhani: (Mph. 5) w05 10/1 23-24 ¶14-15—Mutu: “Opani Mulungu ndi Kumupatsa Ulemelelo.”—Chiv. 14:7. (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 143

  • “Kodi Mwakonzekela Kukumana na Zacipolowe?”: (Mph. 15) Nkhani yokambilana yokambidwa na mkulu. Onetsani vidiyo yakuti Kodi Mwakonzekela Tsoka la Zacilengedwe?. Fotokozani zikumbutso zocokela ku ofesi ya nthambi, komanso za bungwe la akulu ngati zilipo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 05

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 96 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani