LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 12
  • June 20-26

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 20-26
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 12

June 20-26

2 SAMUELI 13-14

  • Nyimbo 127 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Dyela Linamubweletsela Mavuto Aakulu Aminoni”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 14:25, 26​—Kodi nkhani ya Abisalomu itiphunzitsa ciyani za kukongola kwa zoona? (g04 12/22 8-9)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 14:8-20 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno gaŵilani magazini yogwilizana na nkhani imene mwininyumba wayambitsa. (th phunzilo 12)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno itanilani munthuyo ku misonkhano yathu. (th phunzilo 18)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 05 mfundo 6, komanso mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 68

  • “Seŵenzetsani Buku la Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! Pomanga Cikhulupililo mwa Yehova Komanso mwa Yesu.”: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Mangani Cikhulupililo mwa Yehova mwa Kuseŵenzetsa Buku la “Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!” komanso vidiyo yakuti Mangani Cikhulupililo mwa Yesu mwa Kuseŵenzetsa Buku la “Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!”

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 09

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 47 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani