LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 May tsa. 14
  • June 27–July 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 27–July 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 May tsa. 14

June 27–July 3

2 SAMUELI 15-17

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Abisalomu Anapanduka Cifukwa ca Kunyada”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 16:4​—Tingaphunzilepo ciyani pa cigamulo cimene Davide anapanga mosaganizila bwino? (w18.08 6 ¶11)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 17:17-29 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 7)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse) (th phunzilo 2)

  • Nkhani: (Mph. 5) w09 5/15 27-28—Mutu: Tengelani Citsanzo ca Kukangalika kwa Itai pa Utumiki Wanu.—2 Sam. 15:19-22 (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 106

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • “Cikondi . . . Sicidzikuza”: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kumbukilani Mmene Cikondi Cilili—Sicidzikuza.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 10

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 87 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani