LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 July tsa. 4
  • July 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 July tsa. 4

July 11-17

2 SAMUELI 20-21

  • Nyimbo 62 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova ni Mulungu Wacilungamo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Sam. 21:15-17​—Kodi tiphunzilapo zotani pa nkhani imeneyi? (w13 1/15 31 ¶14)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Sam. 20:1-13 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Colinga ca Mulungu—Yes. 55:11. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela mu vidiyo.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kofunsila phunzilo la Baibo. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • “Dziikileni Zolinga za Caka ca Utumiki Catsopano—Katumikilen’koni Kumalo Osowa”: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo—Katumikilenkoni Kumalo Osowa.

  • “Mmene Tingaseŵenzetsele Makambilano Acitsanzo”: (Mph. 5) Nkhani yokambidwa na woyang’anila Msonkhano wa Umoyo na Utumiki.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 12

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 3 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani