August 1-7
1 MAFUMU 1-2
Nyimbo 98 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Maf. 2:37, 41-46—Kodi tiphunzilapo ciyani pa colakwa ca Simeyi? (w05 7/1 30 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Maf. 1:28-40 (th phunzilo 2)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 11)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani za vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (koma musaitambitse). Kenako itanilani mwininyumba ku misonkhano. (th phunzilo 20)
Nkhani: (Mph. 5) km 1/15 2 ¶1-3—Mutu: Phunzilani kwa Ofalitsa Aluso mu Ulaliki. (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Dziikileni Zolinga za Caka ca Utumiki Catsopano—Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu”: (Mph. 7) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo—Funsilani Kuloŵa Sukulu ya Alengezi a Ufumu.
“Dziikileni Zolinga za Caka ca Utumiki Catsopano—Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu”: (Mph. 8) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Loŵani pa Khomo la Zocita Zambili m’Cikhulupililo—Dzipelekeni Kuthandiza pa Nchito Zomanga za Gulu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 14
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 24 na Pemphelo