LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 January tsa. 4
  • January 16-22

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 16-22
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 January tsa. 4

January 16-22

1 MBIRI 1-3

  • Nyimbo 96 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Baibo—Buku Limene Limakamba Zenizeni Osati Nthano”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 1 Mbiri 3:1-3—N’cifukwa ciyani nthawi zina maina a akazi anali kulembedwa m’kaundula wa mibadwo? (it-1 911 ¶3-4)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulila iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Mbiri 1:43-54 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Gaŵilani magazini yofotokoza nkhani imene mwininyumbayo wayambitsa. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 1)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 08 mfundo 7, komanso mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 98

  • “Limbitsani Cikhulupililo Canu pa Mawu a Mulungu”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 34

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 89 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani