LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 March tsa. 14
  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Mukukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Citani Zinthu Mwanzelu Panthawi ya Mtendele
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2020
  • Asa Anacita Zinthu Molimba Mtima—Kodi Inunso Mumatelo?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 March tsa. 14

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Ni Nthawi Iti Pamene Tiyenela Kudalila Yehova?

Asa anadalila Yehova kuti agonjetse gulu lankhondo lalikulu (2 Mbiri 14:9-12; w21.03 5 ¶12)

Patapita nthawi, Asa anadalila Asiriya kuti agonjetse gulu lankhondo laling’ono (2 Mbiri 16:1-3; w21.03 5 ¶13)

Yehova sanakondwele naye Asa cifukwa analeka kudalila thandizo lake (2 Mbiri 16:7-9)

Zithunzi: 1. Mnyamata akubatizika. 2. Mnyamata mmodzimodziyo akusankha pulogilamu imene angatambe pa TV.

Tingadalile Yehova popanga zisankho zikulu-zikulu pa umoyo. Koma tiyenelanso kumudalila popanga zisankho zina. Tiyenela kukumbukila Yehova m’njila zathu zonse.—Miy. 3:5, 6; w21.03 6 ¶14.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani