LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 2
  • May 1-7

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 1-7
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 2

May 1-7

2 MBIRI 17–19

  • Nyimbo 114 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Muziona Ena Mmene Yehova Amawaonela”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 17:9—Kodi tingaphunzilepo ciyani pa nchito yophunzitsa anthu imene Yehosafati anayambitsa? (w17.03 20 ¶10-11)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 17:1-19 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Baibo—Aroma 15:4. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 18)

  • Nkhani: (Mph. 5) w21.05 17-18 ¶11-15 —Mutu: Khalanibe na Maganizo Oyenela Ngati Anthu Alibe Cidwi. (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 104

  • “Muzidziona Mmene Yehova Amakuonelani”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 44 mfundo 5-6, cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 111 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani