LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 4
  • May 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • May 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 4

May 8-14

2 MBIRI 20–21

  • Nyimbo 118 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khulupililani Yehova Mulungu Wanu”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 21:14, 15—Kodi ulosi wa Eliya wokamba za Yehoramu unakwanilitsika bwanji? (it-1 1271 ¶1-2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 20:20-30 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Baibo—Chiv. 21:3, 4. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 9)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 09 cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 119

  • “Kodi Mwakonzeka Kukumana na Mavuto a Zacuma?”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kutamba vidiyo. Ikambidwe na mkulu. Fotokozani zikumbutso zocokela ku ofesi ya nthambi komanso ku bungwe la akulu ngati zilipo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 45 mfundo 1-3

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo Yatsopano ya Msonkhano Wacigawo wa 2023 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani