LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 12
  • June 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 12

June 19-25

2 MBIRI 34-36

  • Nyimbo 97 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mumapindula Nawo Mofikapo Mawu a Mulungu?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • 2 Mbiri 35:20-23—Kodi pali cenjezo lotani pa zimene zinacitikila mfumu yabwino Yosiya? (w17.03 27 ¶15-17)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 2 Mbiri 35:1-14 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana naye mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule Kwambili na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 7)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 11)

  • Nkhani: (Mph. 5) w17.09 25-26 ¶7-10—Mutu: Lolani Mphamvu ya Mawu a Mulungu Kugwila Nchito mu Ulaliki. (th phunzilo 14)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 96

  • “Kodi Mumaigwilitsa Nchito Mofikapo Baibo Yongomvetsela?”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 48 mfundo 5 komanso cidule cake, mafunso obweleza, na colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 117 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani