LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 May tsa. 14
  • June 26–July 2

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • June 26–July 2
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 May tsa. 14

June 26–July 2

EZARA 1-3

  • Nyimbo 75 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Lolani Kuti Yehova Akugwilitseni Nchito”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ezara 1:5, 6—Kodi tiphunzilapo ciyani kwa Aisiraeli ena amene anatsala ku Babulo? (w06 1/15 19 ¶1)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 2:58-70 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki. Koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Ndiyeno m’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 9)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 10 cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • “Pezani Cimwemwe Poyambitsa Makambilano”: (Mph. 15) Kukambilana komanso kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 49 mfundo 1-5

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 132 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani