LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 4
  • July 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 4

July 10-16

EZARA 7-8

  • Nyimbo 82 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalidwe la Ezara Linacititsa Kuti Yehova Alemekezeke”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Ezara 8:1—N’cifukwa ciyani Ayuda ambili ku Babulo sanafune kupita naye Ezara ku Yerusalemu? (w06 1/15 19 ¶10)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Ezara 8:21-36 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Kuvutika—1 Yoh. 5:19. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 59

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 50 mfundo 1-5 komanso vidiyo yakuti Tetezani Ana Anu, imene ili m’bokosi yakuti “Kodi Mudziŵa?”

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 134 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani