LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 6
  • July 24-30

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 24-30
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 6

July 24-30

NEHEMIYA 1-2

  • Nyimbo 47 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nthawi Yomweyo N’napemphela”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 2:4—Kodi iyi inali nthawi yoyamba pamene Nehemiya anapemphela za nkhaniyi? Nanga ife tiphunzilapo ciyani? (w86 2/15 25)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 2:11-20 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 16)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mugaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 tumawu toyamba pa “Kumbani Mozamilapo” na mfundo 4 (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 44

  • Khala Bwenzi la Yehova—Kodi Yehova Amayankha Mapemphelo?: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyoyi. Kenako, funsani omvela funso ili: Kodi vidiyo imeneyi itiphunzitsa ciyani za pemphelo?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 51

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 102 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani