LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 8
  • August 7-13

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 7-13
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 8

August 7-13

NEHEMIYA 5-7

  • Nyimbo 17 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Nehemiya Anali Kufuna Kutumikila Ena, Osati Kutumikilidwa”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 6:13—N’cifukwa ciyani kukanakhala kucimwa Nehemiya akanapita kukabisala m’kacisi? (w07 7/1 30 ¶15)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 5:1-13 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 9)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya! (th phunzilo 6)

  • Nkhani: (Mph. 5) w13 5/15 7 ¶17-19—Mutu: Alaliki Abwino Amathandizana. (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 90

  • “Amagwila Nchito Molimbika Potitumikila”: (Mph. 15) Kukambilana na kuonetsa vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 53

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 35 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani