LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 10
  • August 14-20

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 14-20
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 10

August 14-20

NEHEMIYA 8-9

  • Nyimbo 110 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Cimwemwe Cimene Yehova Amapeleka Ndico Malo Anu Acitetezo”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 8:2, 8—Ngati Aisiraeli anali kukwanitsa “kumvetsela ndi kuzindikila” zimene zinali kuŵelengedwa m’Cilamulo, n’cifukwa ciyani Alevi anali kucifotokozelanso cilamuloco? (it-1 145 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 8:1-12 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni cofalitsa ca m’Thuboksi yathu. (th phunzilo 13)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Ndiyeno chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse) (th phunzilo 11)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 mfundo 5 na mbali yakuti Anthu Ena Amakamba Kuti (th phunzilo 8)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 132

  • “Mungathandize Kuti m’Banja Lanu Mukhale Cimwemwe”: (Mph. 15) Kukambilana na kuonelela vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 54

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani