LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsa. 14
  • August 28–September 3

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • August 28–September 3
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 July tsa. 14

August 28–September 3

NEHEMIYA 12-13

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalani Wokhulupilika kwa Yehova Posankha Mabwenzi”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Neh. 13:10—N’cifukwa ciyani oimba pa kacisi anachulidwa paokha, ngakhale kuti nawonso anali Alevi? (it-2 452 ¶9)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Neh. 12:27-39 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo 16)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kum’patsa kakhadi kopemphela phunzilo la Baibo. (th phunzilo 3)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 11 cidule cake, mafunso obweleza, na colinga (th phunzilo 20)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 108

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5)

  • “Tengelani Cikondi Cosasintha ca Yehova”: (Mph. 10) Kukambilana na kuonelela vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 55 mfundo 5 na cidule cake, mafunso obweleza, komanso colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 84 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani