LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 3
  • September 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 3

September 11-17

ESITERE 3-5

  • Nyimbo 85 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Thandizani Ena Kucita Zonse Zimene Angathe Potumikila Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Esitere 4:​12-16—Kodi timamenyela bwanji ufulu wathu wa kulambila monga anacitila Esitere na Moredekai? (kr 160 ¶14)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 3:​1-12 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Ufumu—Mat 14:​19, 20. Nthawi zonse vidiyo ikaima, inunso iimitseni na kufunsa omvela mafunso amene aonekela.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilani acitsanzo. M’fotokozeleni mmene phunzilo la Baibo limacitikila, na kumusiyila kakhadi kofunsila phunzilo la Baibo. (th phunzilo 16)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 12 ndime yoyamba komanso mfundo 1-3 (th phunzilo 15)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 65

  • Khala Bwenzi la Yehova—Esitere Anali Wolimba Mtima: (Mph. 5) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Ndiyeno ngati n’kotheka, funsani ana amene munawasankhilatu funso ili: Kodi ungakonde kutengela kulimba mtima kwa Esitere m’njila iti?

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 10)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 57

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 125 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani