LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 6
  • September 25–October 1

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 25–October 1
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 6

September 25–October 1

ESITERE 9-10

  • Nyimbo 102 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Anagwilitsa Nchito Udindo Wake Pothandiza Ena”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Esitere 9:​15, 16—N’cifukwa Ciyani Ayuda sanatenge zofunkha? (w06 3/1 11 ¶4)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 9:​1-14 (th phunzilo 11)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pamfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. M’gaŵileni bulosha yakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kumuonetsa mmene phunzilo la Baibo limacitikila. (th phunzilo 13)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 12 Tumawu toyamba pambali yakuti Kumbani Mozamilapo, komanso mfundo 4 (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 117

  • “Abusa Amene Amagwila Nchito Yothandiza Anthu a Yehova”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 59 mfundo 1-5

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 55 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani