LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 8
  • October 2-8

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 2-8
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 8

October 2-8

YOBU 1-3

  • Nyimbo 141 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu pa Yehova”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 1:10—Kodi vesiyi itithandiza bwanji kumvetsa mawu a Yesu a pa Mateyu 27:46? (w21.04 11 ¶9)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 3:​1-26 (th phunzilo  12)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muuzeni za webusaiti yathu na kumusiyila kakhadi koloŵela pa jw.org. (th phunzilo  9)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. ChuIani na kukambilanako vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo  20)

  • Nkhani: (Mph. 5) w22.01 11-12 ¶11-14—Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Muzikamba Mosapita M’mbali Koma Modzicepetsa. (th phunzilo  18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 21

  • N’nali Kuona Kuti Zonse Nikucita Bwino: (Mph. 10) Kukambilana. Tambitsani vidiyoyi. Kenako funsani omvela mafunso otsatilawa: N’cifukwa ciyani M’bale Birdwell anali kuona kuti ‘zonse akucita bwino’?

    Kodi kuganizila lemba la Mateyu 6:33 kunamusintha bwanji?

    N’ciyani cina cimene mwaphunzila pa citsanzo ca banjali?

  • “Seŵenzetsani Tsamba Loyamba la JW.ORG mu Ulaliki”: (Mph. 5) Kukambilana.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 59 mfundo 6 komanso cidule cake, mafunso obweleza na colinga

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 129 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2026)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani