LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 9
  • October 9-15

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 9-15
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 9

October 9-15

YOBU 4-5

  • Nyimbo 121 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Samalani na Nkhani Zabodza”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Yobu 4:4—Ni citsanzo cabwino citi cimene Yobu anapeleka kwa Akhristu masiku ano? (w03 5/15 22 ¶5-6)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Yobu 5:​1-27 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muonetseni mmene angapezele nkhani pa jw.org. (th phunzilo 15)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lff phunzilo 16 mfundo 5 (th phunzilo 16)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 78

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 15)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 60

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 38 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani